Zekariya 11:3 BL92

3 Mau a kucema kwa abusa! pakuti ulemerero wao waipsidwa; mau a kubangula kwa misona ya mikango! pakuti kudzikuza kwa Yordano kwaipsidwa.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 11

Onani Zekariya 11:3 nkhani