Zekariya 12:1 BL92

1 Katundu wa mau a Yehova wakunena Israyeli.Atero Yehova, wakuyala miyamba, ndi kuika maziko a dziko lapansi, ndi kulenga mzimu wa munthu m'kati mwace;

Werengani mutu wathunthu Zekariya 12

Onani Zekariya 12:1 nkhani