17 Tsoka mbusa wopanda pace, wakusiya zoweta! lupanga pa dzanja lace, ndi pa diso lace la kumanja; dzanja lace lidzauma konse, ndi diso lace lamanja lidzada bii.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 11
Onani Zekariya 11:17 nkhani