6 Ndipo wina akati kwa iye, Zipsera izi m'manja mwako nza ciani? adzayankha, Ndizo za mabala anandilasa m'nyumba ya ondikonda.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 13
Onani Zekariya 13:6 nkhani