14 Ndi Yuda yemwe adzacita nkhondo ku Yerusalemu; ndi zolemera za amitundu onse ozungulirapo zidzasonkhanizidwa, golidi, ndi siliva, ndi zobvala zambirimbiri.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 14
Onani Zekariya 14:14 nkhani