Zekariya 14:15 BL92

15 Momwemonso mliri wa pa akavalo, nyuru, ngamila, ndi aburu, ndi nyama zonse zokhala m'misasa iyo, udzakhala ngati mliri uwo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:15 nkhani