Zekariya 14:16 BL92

16 Ndipo kudzacitika kuti otsala onse a amitundu onse anadzawo kulimbana ndi Yerusalemu, adzakwera caka ndi caka kulambira mfumu Yehova wa makamu, ndi kusunga madyerero amisasa.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:16 nkhani