Zekariya 14:17 BL92

17 Ndipo kudzacitika kuti ali yense wa mabanja a dziko wosakwera kumka ku Yerusalemu kulambira mfumu Yehova wa makamu, pa iwowa sipadzakhala mvula.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:17 nkhani