18 Ndipo banja la ku Aigupto likapanda kukwera, losafika, sirdzawagwera kodi mliri umene Yehova adzakantha nao amitundu osakwera kusunga madyerero amisasa?
Werengani mutu wathunthu Zekariya 14
Onani Zekariya 14:18 nkhani