Zekariya 2:4 BL92

4 nanena naye, Thamanga, lankhula ndi mnyamata uyu, ndi kuti, M'Yerusalemu mudzakhala anthu ngati m'midzi yopanda malinga, cifukwa ca kucuruka anthu ndi zoweta momwemo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 2

Onani Zekariya 2:4 nkhani