Zekariya 2:5 BL92

5 Pakuti Ine, ati Yehova, ndidzakhala kwa iye linga lamoto pozungulira pace, ndipo ndidzakhala ulemerero m'kati mwace.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 2

Onani Zekariya 2:5 nkhani