Zekariya 2:6 BL92

6 Haya, haya, thawani ku dziko la kumpoto, ati Yehova; pakuti ndinakubalalitsani ngati mphepo zinai za kuthambo, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 2

Onani Zekariya 2:6 nkhani