Zekariya 2:8 BL92

8 Pakuti atero Yehova wa makamu: Utatha ulemererowo ananditumiza kwa amitundu amene anakufunkhani; pakuti iye wokhudza inu, akhudza mwana wa m'diso lace.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 2

Onani Zekariya 2:8 nkhani