Zekariya 2:9 BL92

9 Pakuti, taonani, ndidzawayambasira dzanja langa, ndipo adzakhala zofunkha za iwo amene anawatumikira; ndipo mudzadziwa kuti Yehova wa makamu anandituma.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 2

Onani Zekariya 2:9 nkhani