Zekariya 4:11 BL92

11 Pamenepo ndinayankha, ndinati kwa iye, Mitengo iyi iwiri ya azitona kulamanja ndi kulamanzere kwa coikapo nyali nciani?

Werengani mutu wathunthu Zekariya 4

Onani Zekariya 4:11 nkhani