Zekariya 4:12 BL92

12 Ndipo ndinayankha kaciwiri, ndinati naye, Nzotani nthambi ziwiri izi za azitona zirikutsanula zokha mafuta onga golidi mwa misiwe iwiri yagolidi?

Werengani mutu wathunthu Zekariya 4

Onani Zekariya 4:12 nkhani