Zekariya 6:5 BL92

5 Ndi mthenga anayankha, nati kwa ine, Izi ndi mphepo zinai zakumwamba zakuturuka kumene zimaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lonse lapansi.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 6

Onani Zekariya 6:5 nkhani