Zekariya 6:6 BL92

6 Gareta wa akavalo akuda aturukira ku dziko la kumpoto; ndi oyerawo aturukira kuwatsata; ndi amawanga aturukira ku dziko la kumwela.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 6

Onani Zekariya 6:6 nkhani