Zekariya 8:2 BL92

2 Atero Yehova wa makamu: Ndimcitira nsanje Ziyoni ndi nsanje yaikuru, ndipo ndimcitira nsanje ndi ukali waukuru.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 8

Onani Zekariya 8:2 nkhani