Zekariya 8:3 BL92

3 Atero Yehova: Ndabwerera kudza ku Ziyoni, ndidzakhala pakati pa Yerusalemu; ndi Yerusalemu adzachedwa, Madzi wa coonadi; ndi phiri la Yehova wa makamu, Phiri lopatulika.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 8

Onani Zekariya 8:3 nkhani