Zekariya 8:22 BL92

22 Inde, mitundu yambiri ya anthu, ndi amitundu amphamvu adzadza kufunafuna Yehova wa makamu m'Yerusalemu, ndi kupepeza Yehova.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 8

Onani Zekariya 8:22 nkhani