Zekariya 9:1 BL92

1 Katundu wa mau a Yehova pa dziko la Hadraki, ndipo Damasiko adzakhala popumula pace; pakuti Yehova apenyerera anthu monga apenyerera mafuko onse a Israyeli;

Werengani mutu wathunthu Zekariya 9

Onani Zekariya 9:1 nkhani