Ahebri 9:11 BL92

11 Koma atafika Kristu, Mkuluwansembe wa zokoma zirinkudza, mwa cihema cacikuru ndi cangwiro coposa, cosamangika ndi manja, ndiko kunena kuti, cosati ca ciiengedweici,

Werengani mutu wathunthu Ahebri 9

Onani Ahebri 9:11 nkhani