Danieli 10:17 BL92

17 Pakuti mnyamata wa mbuye wanga inu akhoza bwanji kulankhula ndi mbuye wanga inu? pakuti ine tsopano apa mulibenso mphamvu mwa ine, osanditsaliranso mpweya.

Werengani mutu wathunthu Danieli 10

Onani Danieli 10:17 nkhani