8 Momwemo ndinatsala ndekha, ndipo ndinaona masomphenya akuruwa, koma wosakhala ndi mphamvu ine; pakuti kukoma kwanga kunasandulika cibvundi mwa ine, wosakhalanso ndi mphamvu ine.
Werengani mutu wathunthu Danieli 10
Onani Danieli 10:8 nkhani