Danieli 11:26 BL92

26 Inde iwo akudyako cakudya cace adzamuononga; ndi ankhondo ace adzasefukira, nadzagwaambiri ophedwa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:26 nkhani