Danieli 11:3 BL92

3 Ndipo idzauka mfumu yamphamvu, nidzacita ufumu ndi ulamuliro waukuru, nidzacita monga mwa cifuniro cace.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:3 nkhani