Danieli 11:37 BL92

37 Ndipo sidzasamalira milungu ya makolo ace, kapena coikhumba akazi, kapena kusamalira milungu iri yonse; pakuti idzadzikuza koposa onse.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:37 nkhani