41 Adzalowanso m'dziko lokometsetsalo ndi maiko ambiri adzapasuka; koma opulumuka dzanja lace ndi awa: Edomu, ndi Moabu, ndi oyamba a ana a Amoni.
Werengani mutu wathunthu Danieli 11
Onani Danieli 11:41 nkhani