Danieli 11:43 BL92

43 Ndipo adzacita mwamphamvu ndi cuma ca golidi, ndi siliva, ndi zinthu zofunika zonse za Aigupto; Alubi ndi Akusi adzatsata mapazi ace.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:43 nkhani