45 Ndipo adzamanga mahema a nyumba yacifumu yace pakati pa nyanja yamcere ndi phiri lopatulika lofunika; koma adzafikira cimariziro cace wopanda wina wakumthandiza.
Werengani mutu wathunthu Danieli 11
Onani Danieli 11:45 nkhani