5 Ndipo mfumu ya kumwela, ndiye wina wa akalonga ace, idzamposa mphamvu, nidzakhala nao ulamuliro; ulamuliro wace ndi ulamuliro waukuru.
Werengani mutu wathunthu Danieli 11
Onani Danieli 11:5 nkhani