Danieli 12:10 BL92

10 Ambiri adzadzitsuka ndi kudziyeretsa, nadzayesedwa ndi moto; koma oipa adzacita moipa; ndipo palibe mmodzi wa oipa adzazindikira; koma aphunzitsi ndiwo adzazindikira.

Werengani mutu wathunthu Danieli 12

Onani Danieli 12:10 nkhani