Danieli 12:3 BL92

3 Ndipo aphunzitsi adzawala ngati kunyezimira kwa thambo; ndi iwo otembenuza ambiri atsate cilungamo ngati nyenyezi ku nthawi za nthawi.

Werengani mutu wathunthu Danieli 12

Onani Danieli 12:3 nkhani