5 Pamenepo ine Danieli ndinapenya, ndipo taonani, anaimapo awiri ena, wina m'mphepete mwa mtsinje tsidya lino, ndi mnzace m'mphepete mwa mtsinje tsidya lija.
Werengani mutu wathunthu Danieli 12
Onani Danieli 12:5 nkhani