18 kuti apemphe zacifundo kwa Mulungu wa Kumwamba pa cinsinsi ici; kuti Danieli ndi anzace asaonongeke pamodzi ndi eni nzeru ena a ku Babulo.
Werengani mutu wathunthu Danieli 2
Onani Danieli 2:18 nkhani