31 Inu mfumu munapenya ndi kuona fano lalikuru. Fanoli linali lalikuru, ndi kunyezimira kwace kunaposa; linali kuima popenyana ndi inu, ndi maonekedwe ace anali oopsa,
Werengani mutu wathunthu Danieli 2
Onani Danieli 2:31 nkhani