Danieli 2:43 BL92

43 Ndi umo mudaonera citsulo cosanganizika ndi dongo, iwo adzadzisokoneza ndi ana a anthu wamba; koma sadzapharikizana, monga umo citsulo sicimasanganizikana ndi dongo.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:43 nkhani