Danieli 2:47 BL92

47 Mfumu inamyankha Danieli, niti, Zoona Mulungu wako ndiye Mulungu wa milungu, ndi Mbuye wa mafumu, ndi wobvumbulutsa zinsinsi; popeza wakhoza kubvumbulutsa cinsinsi ici.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:47 nkhani