14 Nebukadinezara anayankha, nati kwa iwo, Kodi mutero dala, Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, kusatumikira milungu yanga, ndi kusalambira fano lagolidi ndinaliimikalo?
Werengani mutu wathunthu Danieli 3
Onani Danieli 3:14 nkhani