Danieli 3:25 BL92

25 Anayankha, nati, Taonani, ndirikuona amuna anai omasuka, alikuyenda m'kati mwa moto; ndipo alibe kuphwetekwa, ndi maonekedwe a wacinai akunga mwana wa milungu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 3

Onani Danieli 3:25 nkhani