1 Mfumu Belisazara anakonzera anthu ace akulu cikwi cimodzi madyerero akuru, namwa vinyo pamaso pa cikwico.
Werengani mutu wathunthu Danieli 5
Onani Danieli 5:1 nkhani