Danieli 5:15 BL92

15 Ndipo tsono anabwera nao kwa ine anzeru, openda, kuti awerenge lemba ilo, ndi kundidziwitsa kumasulira kwace; koma sanakhoza kufotokozera kumasulira kwa cinthuci.

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:15 nkhani