Danieli 5:29 BL92

29 Pamenepo Belisazara analamulira, ndipo anabveka Danieli cibakuwa, ndi unyolo wagolidi m'khosi mwace, nalalikira za iye kuti ndiye wolamulira wacitatu m'ufumumo.

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:29 nkhani