9 Ndipo mfumu Belisazara anabvutika kwambiri, ndi nkhope yace inasandulika, ndi akuru ace anathedwa nzeru.
Werengani mutu wathunthu Danieli 5
Onani Danieli 5:9 nkhani