Danieli 6:18 BL92

18 Pamenepo mfumu inamuka ku cinyumba cace, nicezera kusala usikuwo, ngakhale zoyimbitsa sanabwera nazo pamaso pace, ndi m'maso mwace munamuumira.

Werengani mutu wathunthu Danieli 6

Onani Danieli 6:18 nkhani