1 Caka coyamba ca Belisazara mfumu ya ku Babulo Danieli anaona loto, naona masomphenya a m'mtima mwace pakama pace; ndipo analemba lotolo, nalifotokozera, mwacidule.
Werengani mutu wathunthu Danieli 7
Onani Danieli 7:1 nkhani