23 Anatero, cirombo cacinai ndico ufumu wacinai pa dziko lapansi, umene udzasiyana nao maufumu onse, nudzalusira dziko lonse lapansi, nudzalipondereza ndi kuliphwanya.
Werengani mutu wathunthu Danieli 7
Onani Danieli 7:23 nkhani