Danieli 7:28 BL92

28 Kutha kwace kwa cinthuci nkuno. Ine Danieli, maganizo anga anandibvuta kwambiri, ndi nkhope yanga inasandulika; koma ndinasunga cinthuci m'mtima mwanga.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:28 nkhani