Danieli 7:6 BL92

6 Pambuyo pace ndinapenya ndi kuona cina ngati nyalugwe, cinali nao mapiko anai a nkhuku pamsana pace, ciromboco cinali nayonso mitu inai, nicinapatsidwa ulamuliro.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:6 nkhani